Miyambo 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kuwala kwa anthu olungama kudzawachititsa kusangalala.+ Koma nyale ya anthu oipa idzazimitsidwa.+