Genesis 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+ Ekisodo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+ Nahumu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Amadzudzula nyanja+ ndi kuiphwetsa ndipo amaumitsa mitsinje yonse.+ Basana ndi Karimeli afota+ ndipo maluwa a mitengo ya ku Lebanoni nawonso afota.
8 Pambuyo pake, Mulungu anakumbukira+ Nowa ndi nyama zonse zakutchire, ndiponso nyama zonse zoweta zimene anali nazo m’chingalawa.+ Ndiyeno Mulungu anachititsa chimphepo kuwomba padziko lapansi, ndipo madzi anayamba kuchepa.+
21 Tsopano Mose anatambasula dzanja lake kuloza panyanja,+ ndipo Yehova anachititsa mphepo yamphamvu yakum’mawa kuyamba kugawa nyanjayo usiku wonse ndi kuumitsa pansi pake.+ Motero madziwo anali kugawikana.+
4 Amadzudzula nyanja+ ndi kuiphwetsa ndipo amaumitsa mitsinje yonse.+ Basana ndi Karimeli afota+ ndipo maluwa a mitengo ya ku Lebanoni nawonso afota.