Genesis 6:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+ 1 Mafumu 8:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la atumiki anu, anthu anu Aisiraeli, popeza mumawaphunzitsa+ njira yabwino yoti ayendemo.+ Mubweretse mvula+ padziko lanu, limene mwapatsa anthu anu monga cholowa. Salimo 104:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kupita kumalo amene munawakonzera.Mapiri anakwera,+Zigwa zinatsika.
17 “Koma ine ndidzabweretsa chigumula+ chamadzi padziko lapansi, kuti chiwononge chamoyo+ chilichonse cha pansi pa thambo, chimene chili ndi mphamvu ya moyo* m’thupi mwake. Chilichonse cha m’dziko lapansi chidzafa.+
36 inuyo mumve muli kumwamba ndipo mukhululuke tchimo la atumiki anu, anthu anu Aisiraeli, popeza mumawaphunzitsa+ njira yabwino yoti ayendemo.+ Mubweretse mvula+ padziko lanu, limene mwapatsa anthu anu monga cholowa.