Yeremiya 14:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo ndikapita kunja kwa mzinda, ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Komanso ndikalowa mkati mwa mzinda ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala.+ Aneneri ndi ansembe, onse ayenda njira zosiyanasiyana kupita kudziko limene sakulidziwa.’”+ Yeremiya 52:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+
18 Ndipo ndikapita kunja kwa mzinda, ndikuona anthu ophedwa ndi lupanga.+ Komanso ndikalowa mkati mwa mzinda ndikuona matenda obwera chifukwa cha njala.+ Aneneri ndi ansembe, onse ayenda njira zosiyanasiyana kupita kudziko limene sakulidziwa.’”+
24 Mkulu wa asilikali olondera mfumu uja anatenganso Seraya+ wansembe wamkulu, Zefaniya+ wansembe wachiwiri, ndi alonda atatu a pakhomo.+