Miyambo 17:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ngakhale munthu wopusa akakhala chete amaoneka ngati wanzeru,+ ndipo wotseka pakamwa pake amaoneka ngati womvetsa zinthu. Yakobo 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+
28 Ngakhale munthu wopusa akakhala chete amaoneka ngati wanzeru,+ ndipo wotseka pakamwa pake amaoneka ngati womvetsa zinthu.
19 Abale anga okondedwa, dziwani izi: Munthu aliyense akhale wofulumira kumva, wodekha polankhula,+ wosafulumira kukwiya,+