Salimo 82:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Kodi mudzaweruza mopanda chilungamo,+Ndi kukondera anthu oipa kufikira liti?+ [Seʹlah.] Yakobo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Koma mukapitiriza kukhala okondera,+ mukuchita tchimo, chifukwa lamulo likukutsutsani+ monga ochimwa.
9 Koma mukapitiriza kukhala okondera,+ mukuchita tchimo, chifukwa lamulo likukutsutsani+ monga ochimwa.