Yobu 19:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ineyo ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Ndipo adzabwera pambuyo panga n’kuimirira+ pafumbi. Salimo 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Pakuti inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+
25 Ineyo ndikudziwa bwino kuti wondiwombola+ ali moyo,Ndipo adzabwera pambuyo panga n’kuimirira+ pafumbi.
4 Ngakhale ndikuyenda m’chigwa cha mdima wandiweyani,+Sindikuopa kanthu,+Pakuti inu muli ndi ine.+Chibonga chanu ndi ndodo yanu ndi zimene zimandilimbikitsa.+