Miyambo 18:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Munthu aliyense woyankhira nkhani asanaimvetsetse n’ngopusa,+ ndipo amachita manyazi.+