Salimo 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+ Salimo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+ Salimo 44:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 N’chifukwa chiyani mukubisabe nkhope yanu?N’chifukwa chiyani mukuiwala masautso athu ndi kuponderezedwa kwathu?+
10 N’chifukwa chiyani inu Yehova mukuima kutali?+N’chifukwa chiyani mukubisala pa nthawi ya masautso?+
13 Kodi mudzandiiwala kufikira liti, inu Yehova?+ Mpaka muyaya?+Mudzandibisira nkhope yanu kufikira liti?+
24 N’chifukwa chiyani mukubisabe nkhope yanu?N’chifukwa chiyani mukuiwala masautso athu ndi kuponderezedwa kwathu?+