Salimo 139:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+ Yeremiya 32:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+
3 Mumandidziwa bwino pamene ndikuyenda komanso pamene ndikugona,+Ndipo njira zanga zonse mukuzidziwa bwino.+
19 Zolinga zanu ndi zazikulu+ ndipo zochita zanu ndi zambiri.+ Maso anu amaona njira zonse za ana a anthu+ kuti munthu aliyense mumuchitire zinthu mogwirizana ndi njira zake komanso zipatso za ntchito zake.+