Salimo 130:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inu Ya, mukanakhala kuti mumayang’anitsitsa zolakwa,+Ndani akanaima pamaso panu, inu Yehova?+