Genesis 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Adamu anagona ndi Hava mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati.+ M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anabereka Kaini*+ n’kunena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna ndi thandizo la Yehova.”+
4 Kenako Adamu anagona ndi Hava mkazi wake, ndipo mkaziyo anatenga pakati.+ M’kupita kwa nthawi, mkaziyo anabereka Kaini*+ n’kunena kuti: “Ndabereka mwana wamwamuna ndi thandizo la Yehova.”+