Yobu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphamvu zake zimachepa,Ndipo tsoka+ limakhala likudikira kuti limuyendetse motsimphina. Yesaya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+ Yuda 13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ali ngatinso mafunde oopsa a panyanja otulutsa thovu la zinthu zoyenera kuwachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zosochera, zimene azisungira mdima wandiweyani wosatha.+
22 Iye adzayang’ana padziko lapansi koma adzangoonapo kuzunzika, mdima,+ kuda, nthawi zovuta ndi zakuda bii, zopanda kuwala.+
13 Ali ngatinso mafunde oopsa a panyanja otulutsa thovu la zinthu zoyenera kuwachititsa manyazi,+ ndiponso nyenyezi zosochera, zimene azisungira mdima wandiweyani wosatha.+