Yobu 18:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mphamvu zake zimachepa,Ndipo tsoka+ limakhala likudikira kuti limuyendetse motsimphina.