Yobu 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chikhale m’manja mwako. Koma iyeyo usam’tambasulire dzanja lako ndi kum’khudza.” Pamenepo Satana anachoka pamaso pa Yehova.+ Yobu 1:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ameneyu ali mkati molankhula kunabwera munthu wina kudzanena kuti: “Kunabwera magulu atatu a Akasidi+ omwe anafika mwaliwiro kwambiri, n’kulanda ngamila ndi kupha abusa ake ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”
12 Choncho Yehova anauza Satana kuti: “Chabwino, chilichonse chimene ali nacho chikhale m’manja mwako. Koma iyeyo usam’tambasulire dzanja lako ndi kum’khudza.” Pamenepo Satana anachoka pamaso pa Yehova.+
17 Ameneyu ali mkati molankhula kunabwera munthu wina kudzanena kuti: “Kunabwera magulu atatu a Akasidi+ omwe anafika mwaliwiro kwambiri, n’kulanda ngamila ndi kupha abusa ake ndi lupanga. Ine ndekha ndi amene ndapulumuka kuti ndidzakuuzeni.”