Salimo 40:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+ Salimo 142:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndinapitirizabe kumukhuthulira nkhawa zanga.+Ndinapitirizabe kumuuza masautso anga.+ Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse, osaleka.+
40 Ndinayembekezera Yehova ndi mtima wonse,+Choncho iye anatchera khutu kwa ine ndipo anamva kufuula kwanga kopempha thandizo.+
2 Ndinapitirizabe kumukhuthulira nkhawa zanga.+Ndinapitirizabe kumuuza masautso anga.+ Luka 18:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndiyeno Yesu anawauza fanizo pofuna kuwasonyeza kufunika koti azipemphera nthawi zonse, osaleka.+