Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Samueli 17:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Kenako Abisalomu ndi amuna onse a Isiraeli anati: “Malangizo a Husai Mwareki ndi abwino+ kusiyana ndi malangizo a Ahitofeli!” Ndipo Yehova anaonetsetsa+ kuti anthuwo asatsatire malangizo+ a Ahitofeli ngakhale kuti anali abwino.+ Yehova anachita zimenezi kuti adzetsere Abisalomu tsoka.+

  • Yesaya 6:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ukachititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+ ndipo ukachititse makutu awo kuti asamamve.+ Ukamate maso awo kuti asamaone ndi maso awowo, ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo, komanso kuti mtima wawo usamvetsetse zinthu, kuti angatembenuke n’kuchira.”+

  • Mateyu 11:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Pa nthawi imeneyo Yesu ananena kuti: “Ndikutamanda inu Atate pamaso pa onse, Ambuye wakumwamba ndi dziko lapansi, chifukwa mwabisira zinthu zimenezi anthu anzeru ndi ozindikira ndipo mwaziulula kwa tiana.+

  • Aroma 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 monga mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tatikulu,+ maso osaona ndi makutu osatha kumva, kufikira lero.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena