Salimo 73:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+ 2 Petulo 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,
22 Ndinakhala wopanda nzeru ndipo sindinadziwe kanthu.+Ndinakhala ngati nyama yakuthengo pamaso panu.+
12 Ndipo anthu amenewa, mofanana ndi nyama zopanda nzeru zimene zimabadwira kuti zidzagwidwe ndi kuwonongedwa, amalankhula monyoza za zinthu zimene sakuzidziwa,+ moti adzawonongedwa chifukwa cha njira yawo yachiwonongeko,