-
Yobu 5:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Zimene iye amakolola, munthu wanjala amazidya.
Ngakhale nyama yake imene waipha n’kuikoloweka pangowe, wina amadzaitenga,
Ndipo msampha umawalanda zofunika pa moyo wawo.
-