Aroma 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti onse ndi ochimwa+ ndipo ndi operewera pa ulemerero wa Mulungu.+