Yobu 3:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa mwamuna wamphamvu amene njira yake yabisika,+Amene Mulungu akum’pingapinga?+ Salimo 88:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+ Maliro 3:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Wanditsekereza ngati mmene mpanda wamiyala umatsekerezera, kuti ndisatuluke.+ Wandimanga ndi maunyolo olemera amkuwa.+
23 N’chifukwa chiyani Mulungu amapereka kuwala kwa mwamuna wamphamvu amene njira yake yabisika,+Amene Mulungu akum’pingapinga?+
8 Anzanga mwawaika kutali ndi ine.+Mwandisandutsa chinthu chonyansa kwa iwo.+Ndatsekerezedwa ndipo sindingathenso kuchoka.+
7 Wanditsekereza ngati mmene mpanda wamiyala umatsekerezera, kuti ndisatuluke.+ Wandimanga ndi maunyolo olemera amkuwa.+