Yesaya 50:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+ Yeremiya 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+
10 Ndani pakati panu amene amaopa+ Yehova ndi kumvera mawu a mtumiki wake?+ Ndani amayenda mu mdima wokhawokha+ ndipo alibe kuwala? Iye akhulupirire dzina la Yehova+ ndipo adalire Mulungu wake.+
16 Patsani Yehova Mulungu wanu ulemerero+ asanachititse mdima,+ komanso mapazi anu asanapunthwe pamapiri madzulo dzuwa litalowa.+ Mudzayembekeza kuwala+ koma iye adzabweretsa mdima,+ ndipo adzachititsa mdima wandiweyani.+