Salimo 31:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+ Salimo 38:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+ Salimo 69:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndadzipatula pakati pa abale anga,+Ndipo ndakhala mlendo pakati pa ana aamuna a mayi anga.+
11 Ndakhala chitonzo+ pamaso pa onse odana nane,+Ndipo kwa anthu oyandikana nawo ndakhala chitonzo chachikulu,+Kwa anthu ondidziwa ndakhala woopsa.+Akandiona ndili panja amandithawa.+
11 Anthu amene anali kundikonda ndiponso anzanga aima patali chifukwa cha kuvutika kwanga,+Ndipo mabwenzi anga apamtima anditalikira.+