2 Mafumu 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Elisa ananyamuka kupita ku Beteli.+ Akuyenda kukwezeka chitunda, anyamata ena+ amene anachokera mumzinda anayamba kumunyoza mokuwa+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe!+ Choka kuno wadazi iwe!”
23 Kenako Elisa ananyamuka kupita ku Beteli.+ Akuyenda kukwezeka chitunda, anyamata ena+ amene anachokera mumzinda anayamba kumunyoza mokuwa+ kuti: “Choka kuno wadazi iwe!+ Choka kuno wadazi iwe!”