Yobu 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Koma tsopano tatambasulani dzanja lanu ndi kukhudza zonse zimene ali nazo, ndipo muona, akutukwanani m’maso muli gwa!”+ Salimo 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Pakuti mivi yanu yandilasa kwambiri,+Ndipo dzanja lanu likundilemera.+
11 Koma tsopano tatambasulani dzanja lanu ndi kukhudza zonse zimene ali nazo, ndipo muona, akutukwanani m’maso muli gwa!”+