Salimo 17:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ine ndidzaona nkhope yanu m’chilungamo.+Podzuka, ndidzakhutira pokuonani.+