Miyambo 16:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova anapanga chilichonse n’cholinga,+ ndipo ngakhale woipa anamusungira tsiku loipa.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+