Yobu 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano linafika tsiku limene ana a Mulungu woona+ ankapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo ngakhalenso Satana+ anapita nawo limodzi.+
6 Tsopano linafika tsiku limene ana a Mulungu woona+ ankapita kukaonekera pamaso pa Yehova,+ ndipo ngakhalenso Satana+ anapita nawo limodzi.+