Yobu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.
10 “Ineyo ndikunyansidwa ndi moyo wanga.+Ndilankhula mwamphamvu za nkhawa zanga.Ndilankhula chifukwa cha kuwawa kwa moyo wanga.