Yobu 31:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Sindikanazengereza kumuuza za mayendedwe anga onse.+Ndikanapita kwa iye ngati kwa mtsogoleri.