Salimo 119:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndasunga mosamala mawu anu mumtima mwanga,+Kuti ndisakuchimwireni.+ Salimo 119:127 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 127 N’chifukwa chake ine ndimakonda malamulo anu+Kuposa golide, golide woyenga bwino.+ Yeremiya 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+
16 Mawu anu anandipeza ndipo ndinawadya.+ Mawu anu amandikondweretsa+ ndi kusangalatsa mtima wanga,+ pakuti ine ndimatchedwa ndi dzina lanu,+ inu Yehova Mulungu wa makamu.+