Yesaya 26:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+
10 Ngakhale munthu woipa atachitiridwa zabwino, sangaphunzire chilungamo.+ M’dziko lochita zowongoka, iye adzachita zinthu zopanda chilungamo+ ndipo sadzaona ukulu wa Yehova.+