Ekisodo 22:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Anthu inu musazunze mkazi wamasiye kapena mwana wamasiye* aliyense.+ Zekariya 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+
10 Musamabere mwachinyengo mkazi wamasiye,+ mwana wamasiye,*+ mlendo+ kapena munthu wosautsika.+ Musamakonzerane chiwembu mumtima mwanu.’+