Danieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+
3 Zizindikiro zake n’zazikulu ndipo zodabwitsa zake n’zamphamvu.+ Ufumu wake udzakhalapo mpaka kalekale+ ndipo ulamuliro wake udzakhalapo ku mibadwomibadwo.+