Ekisodo 34:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pamenepo Yehova anatsika+ mumtambo ndi kuimirira pafupi ndi Mose, n’kulengeza dzina lake lakuti Yehova.+ Salimo 97:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+
5 Pamenepo Yehova anatsika+ mumtambo ndi kuimirira pafupi ndi Mose, n’kulengeza dzina lake lakuti Yehova.+
2 Mitambo ndi mdima wandiweyani zamuzungulira.+Chilungamo ndi chiweruzo ndizo malo okhazikika a mpando wake wachifumu.+