Mateyu 7:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiye kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinafika n’kuwomba nyumbayo+ moti inagwa, ndipo kugwa kwake kunali kwakukulu.”+
27 Ndiye kunagwa chimvula champhamvu ndipo madzi anasefukira. Kenako chimphepo chinafika n’kuwomba nyumbayo+ moti inagwa, ndipo kugwa kwake kunali kwakukulu.”+