Genesis 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pamenepo Yehova anati: “Taonani! Izi n’zimene anthuwa ayamba kuchita popeza ndi amodzi ndipo onse ali ndi chilankhulo chimodzi.+ Mmene zililimu, angathe kuchita chilichonse chimene akuganiza.+ Luka 1:51 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 51 Wachita zamphamvu ndi dzanja lake,+ wabalalitsira kutali odzikweza m’zolinga za mitima yawo.+
6 Pamenepo Yehova anati: “Taonani! Izi n’zimene anthuwa ayamba kuchita popeza ndi amodzi ndipo onse ali ndi chilankhulo chimodzi.+ Mmene zililimu, angathe kuchita chilichonse chimene akuganiza.+