Levitiko 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Komanso mtundu uliwonse wa mphamba wofiira ndi mphamba wakuda,+ Deuteronomo 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 mphamba wofiira, mphamba wakuda+ ndi mtundu uliwonse wa kamtema.