2 Mafumu 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Nkhani zina zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso mmene anakumbira dziwe+ ndi ngalande+ n’kubweretsa madzi mumzindawo, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda. 2 Mbiri 32:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+
20 Nkhani zina zokhudza Hezekiya ndi zochita zake zonse zamphamvu, ndiponso mmene anakumbira dziwe+ ndi ngalande+ n’kubweretsa madzi mumzindawo, zinalembedwa m’buku+ la zochitika za m’masiku a mafumu a Yuda.
30 Hezekiya ndiye anatseka+ kasupe wapamtunda wa madzi+ a ku Gihoni+ ndipo anawapatutsa n’kuwalunjikitsa kumunsi kumadzulo, ku Mzinda wa Davide.+ Ntchito iliyonse imene Hezekiya anali kuchita inali kumuyendera bwino.+