Salimo 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola m’bale wake,+Kapena kumuperekera dipo* kwa Mulungu, Miyambo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zonse zimene umakonda sizingafanane nazo.
7 Palibe ngakhale mmodzi wa iwo amene angathe kuwombola m’bale wake,+Kapena kumuperekera dipo* kwa Mulungu, Miyambo 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’zamtengo wapatali kuposa miyala ya korali,+ ndipo zonse zimene umakonda sizingafanane nazo.