Mlaliki 11:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho chotsa zosautsa mumtima mwako ndipo teteza thupi lako ku tsoka,+ chifukwa unyamata ndiponso pachimake pa moyo n’zachabechabe.+
10 Choncho chotsa zosautsa mumtima mwako ndipo teteza thupi lako ku tsoka,+ chifukwa unyamata ndiponso pachimake pa moyo n’zachabechabe.+