-
Numeri 10:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 Komabe Mose anam’pempha kuti: “Chonde musatisiye, pakuti inu mukudziwa bwino kumene tingamange msasa m’chipululu muno, ndipo mungakhale maso athu.
-