Luka 14:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma ukakonza phwando, uziitana anthu osauka, otsimphina, olumala, ndi akhungu.+ Yakobo 1:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+
27 Kupembedza koyera+ ndi kosaipitsidwa+ kwa Mulungu ndi Atate wathu ndi uku: Kusamalira ana amasiye+ ndi akazi amasiye+ m’masautso awo,+ ndi kukhala wopanda banga+ la dzikoli.+