Yobu 16:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndamva zinthu zambiri ngati zimenezi.Nonsenu ndinu otonthoza onditopetsa!+ Salimo 69:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa.
26 Pakuti iwo amalondalonda munthu amene inu mwamulanga,+Ndipo amakamba za ululu wa anthu amene inu mwawalasa.