Yobu 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu? Yobu 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+
20 Ngati ndachimwa, ndingakuchiteni chiyani Inu amene mumaonetsetsa anthu?+N’chifukwa chiyani mwalunjika ine, kuti ndikhale cholemetsa kwa inu?
6 Dziwani kuti Mulungu mwiniwakeyo ndi amene wandisocheretsa,Ndipo wandizunguliza ndi ukonde wake wosakira nyama.+