Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu,+ poti palibe wina wokhala ngati iyeyo padziko lapansi? Iyetu ndi munthu wopanda cholakwa ndi wowongoka mtima,+ woopa Mulungu+ ndiponso wopewa zoipa.+ Komabe iye akadali ndi mtima wosagawanika+ ngakhale kuti iweyo ukundiumiriza+ kuti ndimuwononge popanda chifukwa.”+

  • Yobu 27:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Inetu sindingayerekeze n’komwe kunena kuti amuna inu ndinu olungama.+

      Mpaka ine kumwalira, sindidzasiya kukhala ndi mtima wosagawanika.+

  • Salimo 7:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Yehova adzapereka chigamulo ku mitundu ya anthu.+

      Ndiweruzeni inu Yehova, mogwirizana ndi chilungamo changa,+

      Komanso mogwirizana ndi mtima wanga wosagawanika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena