Salimo 82:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chitirani chilungamo anthu onyozeka ndi ana amasiye.*+Chitirani chilungamo anthu osautsika ndi osauka.+ Miyambo 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Pakuti Yehova adzawateteza pa mlandu wawo,+ ndipo adzalanda moyo wa amene akuwabera.+ Yesaya 10:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+
3 Chitirani chilungamo anthu onyozeka ndi ana amasiye.*+Chitirani chilungamo anthu osautsika ndi osauka.+
3 Kodi anthu inu mudzatani pa tsiku limene adzatembenukire kwa inu+ ndi kukubweretserani chiwonongeko chochokera kutali?+ Mudzathawira kwa ndani kuti akuthandizeni+ ndipo ulemerero wanu mudzausiya kuti?+