Yesaya 24:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+
8 Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi maseche zasiya kumveka. Phokoso la anthu okondwa kwambiri silikumvekanso. Nyimbo zachisangalalo zoimbidwa ndi zeze zaleka kumveka.+