Deuteronomo 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+
16 Samalani kuti mitima yanu isakopeke+ ndipo musapatuke ndi kupembedza milungu ina n’kumaiweramira.+