Mateyu 5:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Koma ine ndikukuuzani kuti: Pitirizani kukonda adani anu+ ndi kupempherera amene akukuzunzani,+ Aroma 12:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitirizani kudalitsa anthu amene amakuzunzani.+ Muzidalitsa,+ osatemberera ayi.+